Yoswa 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Malirewo anapitirira mpaka ku Beti-hogila+ nʼkukadutsa kumpoto kwa Beti-araba,+ kukafika kumwala wa Bohani,+ mwana wa Rubeni. Yoswa 15:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Malire akumadzulo anali Nyanja Yaikulu*+ ndi gombe lake. Amenewa anali malire a ana a Yuda a mbali zonse motsatira mabanja awo.
6 Malirewo anapitirira mpaka ku Beti-hogila+ nʼkukadutsa kumpoto kwa Beti-araba,+ kukafika kumwala wa Bohani,+ mwana wa Rubeni.
12 Malire akumadzulo anali Nyanja Yaikulu*+ ndi gombe lake. Amenewa anali malire a ana a Yuda a mbali zonse motsatira mabanja awo.