Yoswa 20:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho anasankha mizinda ina kuti ikhale yopatulika. Mizinda yake inali Kedesi+ ku Galileya mʼdera lamapiri la Nafitali, Sekemu+ mʼdera lamapiri la Efuraimu komanso Kiriyati-ariba,+ kutanthauza Heburoni, mʼdera lamapiri la Yuda.
7 Choncho anasankha mizinda ina kuti ikhale yopatulika. Mizinda yake inali Kedesi+ ku Galileya mʼdera lamapiri la Nafitali, Sekemu+ mʼdera lamapiri la Efuraimu komanso Kiriyati-ariba,+ kutanthauza Heburoni, mʼdera lamapiri la Yuda.