Genesis 32:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yakobo atangowaona anati: “Ilitu ndi gulu la Mulungu!” Choncho malowo anawatchula kuti Mahanaimu.* 2 Samueli 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma Abineri+ mwana wa Nera, amene anali mtsogoleri wa asilikali a Sauli, anatenga Isi-boseti,+ mwana wa Sauli, nʼkupita naye ku Mahanaimu.+
8 Koma Abineri+ mwana wa Nera, amene anali mtsogoleri wa asilikali a Sauli, anatenga Isi-boseti,+ mwana wa Sauli, nʼkupita naye ku Mahanaimu.+