Yoswa 21:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Yehova anachititsa kuti azikhala mwamtendere mʼdzikolo, mogwirizana ndi zonse zimene analumbirira makolo awo.+ Panalibe mdani aliyense amene anatha kulimbana nawo.+ Yehova anapereka adani awo onse mʼmanja mwawo.+
44 Yehova anachititsa kuti azikhala mwamtendere mʼdzikolo, mogwirizana ndi zonse zimene analumbirira makolo awo.+ Panalibe mdani aliyense amene anatha kulimbana nawo.+ Yehova anapereka adani awo onse mʼmanja mwawo.+