Deuteronomo 4:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mukadzafufuza Yehova Mulungu wanu muli kumeneko, mukadzamufunafuna ndi mtima wanu wonse komanso moyo wanu wonse, mudzamupezadi.+ Deuteronomo 11:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndiyeno mukadzamvera mokhulupirika malamulo anga amene ndikukupatsani lero, komanso kukonda Yehova Mulungu wanu nʼkumamutumikira ndi mtima wanu wonse, ndi moyo wanu wonse,+ Maliko 12:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Muzikonda Yehova* Mulungu wanu ndi mtima wanu wonse, moyo wanu wonse, maganizo anu onse ndi mphamvu zanu zonse.’+ Maliko 12:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ndipo kukonda Mulungu ndi mtima wonse, maganizo onse, mphamvu zonse komanso kukonda mnzako mmene umadzikondera wekha, nʼzofunika kwambiri kuposa nsembe zonse zopsereza zathunthu ndi nsembe zina.”+
29 Mukadzafufuza Yehova Mulungu wanu muli kumeneko, mukadzamufunafuna ndi mtima wanu wonse komanso moyo wanu wonse, mudzamupezadi.+
13 Ndiyeno mukadzamvera mokhulupirika malamulo anga amene ndikukupatsani lero, komanso kukonda Yehova Mulungu wanu nʼkumamutumikira ndi mtima wanu wonse, ndi moyo wanu wonse,+
30 Muzikonda Yehova* Mulungu wanu ndi mtima wanu wonse, moyo wanu wonse, maganizo anu onse ndi mphamvu zanu zonse.’+
33 Ndipo kukonda Mulungu ndi mtima wonse, maganizo onse, mphamvu zonse komanso kukonda mnzako mmene umadzikondera wekha, nʼzofunika kwambiri kuposa nsembe zonse zopsereza zathunthu ndi nsembe zina.”+