Oweruza 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pa nthawiyi nʼkuti Zeba ndi Zalimuna ali ku Karikori pamodzi ndi asilikali awo pafupifupi 15,000. Asilikaliwa ndi amene anatsala pa gulu lonse la asilikali a Kumʼmawa+ chifukwa asilikali 120,000 anali ataphedwa.
10 Pa nthawiyi nʼkuti Zeba ndi Zalimuna ali ku Karikori pamodzi ndi asilikali awo pafupifupi 15,000. Asilikaliwa ndi amene anatsala pa gulu lonse la asilikali a Kumʼmawa+ chifukwa asilikali 120,000 anali ataphedwa.