Oweruza 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Amidiyaniwo anayamba kupondereza Aisiraeli.+ Chifukwa cha zimenezi, Aisiraeli anakonza malo oti azibisalako* mʼmapiri, mʼmapanga ndi mʼmalo ena ovuta kufikako.+
2 Amidiyaniwo anayamba kupondereza Aisiraeli.+ Chifukwa cha zimenezi, Aisiraeli anakonza malo oti azibisalako* mʼmapiri, mʼmapanga ndi mʼmalo ena ovuta kufikako.+