-
Genesis 18:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Ndiyeno anati: “Yehova, ngati mungandikomere mtima, chonde, musangondipitirira ine mtumiki wanu.
-
-
Genesis 18:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Popeza mwafika kwa mtumiki wanu, ndiloleni ndikubweretsereni kachakudya kuti mupezenso mphamvu. Kenako mukhoza kupitiriza ulendo wanu.” Pamenepo iwo anati: “Chabwino, chita mmene waneneramo.”
-