Oweruza 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako, kunabwera mngelo wa Yehova+ nʼkukhala pansi pa mtengo waukulu ku Ofira. Mtengo umenewu unali wa Yowasi, Mwabi-ezeri.+ Pa nthawiyi, Gidiyoni+ mwana wa Yowasi, ankapuntha tirigu moponderamo mphesa kuti Amidiyani asaone. Oweruza 6:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Pa tsikuli Yowasi anapatsa Gidiyoni dzina lakuti Yerubaala* nʼkunena kuti: “Baala adziteteze yekha, chifukwa munthu wina wamugwetsera guwa lake lansembe.”
11 Kenako, kunabwera mngelo wa Yehova+ nʼkukhala pansi pa mtengo waukulu ku Ofira. Mtengo umenewu unali wa Yowasi, Mwabi-ezeri.+ Pa nthawiyi, Gidiyoni+ mwana wa Yowasi, ankapuntha tirigu moponderamo mphesa kuti Amidiyani asaone.
32 Pa tsikuli Yowasi anapatsa Gidiyoni dzina lakuti Yerubaala* nʼkunena kuti: “Baala adziteteze yekha, chifukwa munthu wina wamugwetsera guwa lake lansembe.”