Oweruza 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako, kunabwera mngelo wa Yehova+ nʼkukhala pansi pa mtengo waukulu ku Ofira. Mtengo umenewu unali wa Yowasi, Mwabi-ezeri.+ Pa nthawiyi, Gidiyoni+ mwana wa Yowasi, ankapuntha tirigu moponderamo mphesa kuti Amidiyani asaone. Oweruza 6:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Choncho, Gidiyoni anamangira Yehova guwa lansembe pamalowo, ndipo limatchedwa Yehova-salomu*+ mpaka pano. Guwalo lili ku Ofira, mzinda wa Aabi-ezeri, mpaka pano.
11 Kenako, kunabwera mngelo wa Yehova+ nʼkukhala pansi pa mtengo waukulu ku Ofira. Mtengo umenewu unali wa Yowasi, Mwabi-ezeri.+ Pa nthawiyi, Gidiyoni+ mwana wa Yowasi, ankapuntha tirigu moponderamo mphesa kuti Amidiyani asaone.
24 Choncho, Gidiyoni anamangira Yehova guwa lansembe pamalowo, ndipo limatchedwa Yehova-salomu*+ mpaka pano. Guwalo lili ku Ofira, mzinda wa Aabi-ezeri, mpaka pano.