Oweruza 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno anthu ndi akalonga a Giliyadi anayamba kufunsana kuti: “Ndani atitsogolere kukamenyana ndi Aamoni?+ Ameneyo akhale mtsogoleri wa anthu onse okhala mʼGiliyadi.”
18 Ndiyeno anthu ndi akalonga a Giliyadi anayamba kufunsana kuti: “Ndani atitsogolere kukamenyana ndi Aamoni?+ Ameneyo akhale mtsogoleri wa anthu onse okhala mʼGiliyadi.”