-
Yoswa 17:14, 15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Ana a Yosefe anafunsa Yoswa kuti: “Nʼchifukwa chiyani mwatipatsa gawo limodzi lokha+ kuti likhale cholowa chathu, pomwe tilipo anthu ambiri popeza Yehova akutidalitsabe mpaka pano?”+ 15 Yoswa anawayankha kuti: “Ngati mulipo ambiri pitani kumtunda kunkhalango ya Aperezi+ ndi ya Arefai,+ mukagwetse mitengo nʼkutenga deralo, poti dera lamapiri la Efuraimu+ lakucheperani.”
-