Oweruza 20:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiyeno Aisiraeli anapita ku Beteli ndipo analira pamaso pa Yehova mpaka madzulo. Iwo anafunsa Yehova kuti: “Kodi tipitenso kukamenyana ndi abale athu a fuko la Benjamini?”+ Yehova anawayankha kuti: “Pitani mukamenyane nawo.”
23 Ndiyeno Aisiraeli anapita ku Beteli ndipo analira pamaso pa Yehova mpaka madzulo. Iwo anafunsa Yehova kuti: “Kodi tipitenso kukamenyana ndi abale athu a fuko la Benjamini?”+ Yehova anawayankha kuti: “Pitani mukamenyane nawo.”