-
Rute 2:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Pa nthawi ya chakudya Boazi anauza Rute kuti: “Bwera kuno udzadye mkate. Ukhozanso kumasunsa mu vinyo wowawasayu.” Choncho Rute anapita nʼkukakhala pansi limodzi ndi okololawo. Ndiyeno Boazi ankamupatsa balere wokazinga ndipo iye anadya nʼkukhuta mpaka wina kutsala.
-