-
Deuteronomo 25:5, 6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Ngati amuna apachibale akukhala moyandikana, ndiyeno mmodzi nʼkumwalira asanabereke mwana wamwamuna, mkazi wa womwalirayo asakwatiwe ndi mwamuna wochokera mʼbanja lina. Mlamu wake azipita kwa iye nʼkukamutenga kukhala mkazi wake, ndipo azichita ukwati wa pachilamu.+ 6 Mwana woyamba amene mkaziyo angabereke, azitenga dzina la mwamuna womwalira uja,+ kuti dzina la mʼbale wake lisathe mu Isiraeli.+
-