Ekisodo 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ine ndidzadutsa mʼdziko la Iguputo usiku umenewo nʼkupha mwana aliyense woyamba kubadwa mʼdziko la Iguputo, mwana wa munthu kapena wa chiweto.+ Ndipo ndidzapereka chiweruzo pa milungu yonse ya mu Iguputo.+ Ine ndine Yehova. 1 Mbiri 16:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Milungu yonse ya anthu a mitundu ina ndi milungu yopanda pake.+Koma Yehova ndi amene anapanga kumwamba.+ Salimo 97:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Onse amene akutumikira chifaniziro chilichonse achite manyazi,+Amene amadzitama chifukwa cha milungu yawo yopanda pake.+ Muweramireni,* inu milungu yonse.+
12 Ine ndidzadutsa mʼdziko la Iguputo usiku umenewo nʼkupha mwana aliyense woyamba kubadwa mʼdziko la Iguputo, mwana wa munthu kapena wa chiweto.+ Ndipo ndidzapereka chiweruzo pa milungu yonse ya mu Iguputo.+ Ine ndine Yehova.
26 Milungu yonse ya anthu a mitundu ina ndi milungu yopanda pake.+Koma Yehova ndi amene anapanga kumwamba.+
7 Onse amene akutumikira chifaniziro chilichonse achite manyazi,+Amene amadzitama chifukwa cha milungu yawo yopanda pake.+ Muweramireni,* inu milungu yonse.+