Ekisodo 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ngakhale zinali choncho, Farao anaumitsabe mtima wake+ ndipo sanawamvere, mogwirizana ndi zimene Yehova ananena. Ekisodo 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Farao ataona kuti mliri wa achulewo watha, anaumitsa mtima wake,+ ndipo sanamvere Mose ndi Aroni, mogwirizana ndi zimene Yehova ananena. Ekisodo 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma ine ndilola kuti Aiguputo aumitse mitima yawo, moti atsatira Aisiraeli panyanjapo. Ndichita zimenezi kuti ndilemekeze dzina langa pogonjetsa Farao, gulu lake lonse lankhondo, magaleta ake ankhondo ndi asilikali ake apamahatchi.+
13 Ngakhale zinali choncho, Farao anaumitsabe mtima wake+ ndipo sanawamvere, mogwirizana ndi zimene Yehova ananena.
15 Farao ataona kuti mliri wa achulewo watha, anaumitsa mtima wake,+ ndipo sanamvere Mose ndi Aroni, mogwirizana ndi zimene Yehova ananena.
17 Koma ine ndilola kuti Aiguputo aumitse mitima yawo, moti atsatira Aisiraeli panyanjapo. Ndichita zimenezi kuti ndilemekeze dzina langa pogonjetsa Farao, gulu lake lonse lankhondo, magaleta ake ankhondo ndi asilikali ake apamahatchi.+