17 Ponena za Farao, lemba lina linati: “Ndakusiya ndi moyo kuti ndikusonyeze mphamvu zanga komanso kuti dzina langa lilengezedwe padziko lonse lapansi.”+ 18 Choncho iye amachitira chifundo munthu amene wafuna kumuchitira chifundo, koma amalola anthu ena kuti aumitse mitima yawo.+