1 Samueli 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno Samueli anatenga botolo ladothi lomwe munali mafuta nʼkuthira mafutawo pamutu pa Sauli.+ Kenako anamukisa nʼkunena kuti: “Yehova wakudzoza kuti ukhale mtsogoleri+ wa anthu ake.*+ 1 Samueli 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno Samueli anauza Sauli kuti: “Yehova anandituma kudzakudzoza kuti ukhale mfumu ya anthu ake Aisiraeli.+ Ndiye tamvera zimene Yehova wanena.+
10 Ndiyeno Samueli anatenga botolo ladothi lomwe munali mafuta nʼkuthira mafutawo pamutu pa Sauli.+ Kenako anamukisa nʼkunena kuti: “Yehova wakudzoza kuti ukhale mtsogoleri+ wa anthu ake.*+
15 Ndiyeno Samueli anauza Sauli kuti: “Yehova anandituma kudzakudzoza kuti ukhale mfumu ya anthu ake Aisiraeli.+ Ndiye tamvera zimene Yehova wanena.+