Numeri 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mose atamva zimenezi anakwiya kwambiri ndipo anauza Yehova kuti: “Nsembe zawo zambewu musaziyangʼane. Ine sindinawalande ngakhale bulu mmodzi, kapena kuchitira aliyense wa anthuwo chinthu choipa.”+
15 Mose atamva zimenezi anakwiya kwambiri ndipo anauza Yehova kuti: “Nsembe zawo zambewu musaziyangʼane. Ine sindinawalande ngakhale bulu mmodzi, kapena kuchitira aliyense wa anthuwo chinthu choipa.”+