-
1 Samueli 14:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Sauli anauza anthu amene anali naye kuti: “Werengani anthu kuti muone amene wachoka.” Atawerenga anthuwo, anapeza kuti Yonatani ndi womunyamulira zida palibe.
-