-
1 Mafumu 2:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Iweyo ukudziwa bwino zimene Yowabu mwana wa Zeruya anandichitira, anapha akulu awiri a asilikali a Isiraeli, Abineri+ mwana wa Nera ndi Amasa+ mwana wa Yeteri. Iye anakhetsa magazi+ ankhondo pa nthawi yamtendere. Ndipo anadetsa ndi magazi ankhondo lamba amene anali mʼchiuno mwake ndiponso nsapato zimene zinali kuphazi kwake.
-