Levitiko 27:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kuwonjezera pamenepa, munthu aliyense amene waperekedwa kwa Mulungu kuti awonongedwe sangathe kuwomboledwa.+ Ameneyo aziphedwa ndithu.+ 1 Samueli 15:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako Yehova anakutuma kuti, ‘Pita ukaphe anthu ochimwa, Aamaleki.+ Ukamenyane nawo mpaka ukawaphe onse.’+
29 Kuwonjezera pamenepa, munthu aliyense amene waperekedwa kwa Mulungu kuti awonongedwe sangathe kuwomboledwa.+ Ameneyo aziphedwa ndithu.+
18 Kenako Yehova anakutuma kuti, ‘Pita ukaphe anthu ochimwa, Aamaleki.+ Ukamenyane nawo mpaka ukawaphe onse.’+