Deuteronomo 13:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Dzanja lanu lisatenge chinthu chilichonse choyenera kuwonongedwa,+ kuti mkwiyo woyaka moto wa Yehova usiye kukuyakirani ndiponso kuti akuchitireni chifundo, kukumverani chisoni ndi kukuchulukitsani, mogwirizana ndi zimene analumbira kwa makolo anu.+ 1 Samueli 15:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Sauli ndi anthu ake anasiya* Agagi, nkhosa ndi ngʼombe zabwino kwambiri, ziweto zonenepa, nkhosa zamphongo ndi zina zonse zimene zinali zabwino.+ Iwo sanafune kupha zimenezi, koma zinthu zonse zimene zinali zachabechabe ndi zosafunika anaziwononga.
17 Dzanja lanu lisatenge chinthu chilichonse choyenera kuwonongedwa,+ kuti mkwiyo woyaka moto wa Yehova usiye kukuyakirani ndiponso kuti akuchitireni chifundo, kukumverani chisoni ndi kukuchulukitsani, mogwirizana ndi zimene analumbira kwa makolo anu.+
9 Sauli ndi anthu ake anasiya* Agagi, nkhosa ndi ngʼombe zabwino kwambiri, ziweto zonenepa, nkhosa zamphongo ndi zina zonse zimene zinali zabwino.+ Iwo sanafune kupha zimenezi, koma zinthu zonse zimene zinali zachabechabe ndi zosafunika anaziwononga.