-
1 Samueli 17:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Eliyabu+ mchimwene wake wamkulu wa Davide atamva Davideyo akulankhula ndi anthuwo, anapsa naye mtima kwambiri. Iye anati: “Wabwera kudzatani kuno? Nanga nkhosa zochepa zija wasiyira ndani kuchipululu?+ Ine ndikudziwa bwino kuti ndiwe wodzikuza komanso uli ndi maganizo olakwika. Iweyo wabwera kuno kuti udzaone mmene nkhondo ikuyendera.”
-