1 Samueli 10:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kenako anabweretsa pafupi fuko la Benjamini potengera mabanja awo ndipo banja la Amatiri linasankhidwa. Pomaliza, Sauli mwana wa Kisi anasankhidwa.+ Koma atamufufuza, sanamupeze. 1 Samueli 10:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Choncho anthu anathamanga nʼkukamutenga. Ataimirira pakati pa anthuwo, ankaoneka wamtali kwambiri moti palibe aliyense amene ankapitirira mʼmapewa ake.+
21 Kenako anabweretsa pafupi fuko la Benjamini potengera mabanja awo ndipo banja la Amatiri linasankhidwa. Pomaliza, Sauli mwana wa Kisi anasankhidwa.+ Koma atamufufuza, sanamupeze.
23 Choncho anthu anathamanga nʼkukamutenga. Ataimirira pakati pa anthuwo, ankaoneka wamtali kwambiri moti palibe aliyense amene ankapitirira mʼmapewa ake.+