1 Samueli 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pa nthawiyi Eli anali atakalamba kwambiri koma anamva zonse zimene ana ake ankachitira+ Aisiraeli onse. Anamvanso kuti ankagona ndi akazi amene ankatumikira pakhomo la chihema chokumanako.+
22 Pa nthawiyi Eli anali atakalamba kwambiri koma anamva zonse zimene ana ake ankachitira+ Aisiraeli onse. Anamvanso kuti ankagona ndi akazi amene ankatumikira pakhomo la chihema chokumanako.+