Numeri 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Uike Aroni ndi ana ake kuti akhale ansembe, ndipo azigwira ntchito zawo zaunsembe.+ Munthu wamba* aliyense amene wayandikira malowo, aziphedwa.”+ Deuteronomo 33:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Amenewa azilangiza Yakobo pa zigamulo zanu+Ndi Isiraeli mʼChilamulo chanu.+ Azipereka nsembe zofukiza kuti zikhale kafungo kosangalatsa kwa inu,*+Ndi nsembe yathunthu paguwa lanu lansembe.+ Malaki 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Wansembe ayenera kuphunzitsa anthu za Mulungu. Anthu ayenera kupita kwa iye kuti akamve Chilamulo*+ chifukwa iye ndi mthenga wa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.
10 Uike Aroni ndi ana ake kuti akhale ansembe, ndipo azigwira ntchito zawo zaunsembe.+ Munthu wamba* aliyense amene wayandikira malowo, aziphedwa.”+
10 Amenewa azilangiza Yakobo pa zigamulo zanu+Ndi Isiraeli mʼChilamulo chanu.+ Azipereka nsembe zofukiza kuti zikhale kafungo kosangalatsa kwa inu,*+Ndi nsembe yathunthu paguwa lanu lansembe.+
7 Wansembe ayenera kuphunzitsa anthu za Mulungu. Anthu ayenera kupita kwa iye kuti akamve Chilamulo*+ chifukwa iye ndi mthenga wa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.