1 Samueli 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Samueli anatenga nyanga ya mafuta+ nʼkumudzoza azichimwene ake akuona. Kuyambira tsiku limenelo, mzimu wa Yehova unayamba kuthandiza Davide.+ Kenako Samueli anabwerera ku Rama.+ 1 Samueli 24:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iye anauza Davide kuti: “Ndiwe wolungama kwambiri kuposa ine, chifukwa wandichitira zabwino, koma ine ndakubwezera zoipa.+ 1 Samueli 24:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ine ndikudziwa kuti iweyo udzakhala mfumu,+ ndipo ufumu wa Isiraeli udzakhalabe mʼmanja mwako.
13 Samueli anatenga nyanga ya mafuta+ nʼkumudzoza azichimwene ake akuona. Kuyambira tsiku limenelo, mzimu wa Yehova unayamba kuthandiza Davide.+ Kenako Samueli anabwerera ku Rama.+
17 Iye anauza Davide kuti: “Ndiwe wolungama kwambiri kuposa ine, chifukwa wandichitira zabwino, koma ine ndakubwezera zoipa.+