13 Umuuze kuti ndidzaweruza nyumba yake mpaka kalekale chifukwa cha zinthu zolakwika zimene iye akuzidziwa.+ Ana ake akunyoza Mulungu+ koma sakuwadzudzula.+ 14 Nʼchifukwa chake ndalumbirira nyumba ya Eli kuti machimo a anthu a mʼnyumba ya Eli sadzaphimbidwa ndi nsembe ina iliyonse.”+