1 Samueli 20:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Davide anauza Yonatani kuti: “Paja mawa ndi tsiku limene mwezi watsopano uoneke,+ ndipo ndiyenera kukadya ndi mfumu. Ndimati undilole ndipite kukabisala kutchire mpaka mkuja madzulo.
5 Davide anauza Yonatani kuti: “Paja mawa ndi tsiku limene mwezi watsopano uoneke,+ ndipo ndiyenera kukadya ndi mfumu. Ndimati undilole ndipite kukabisala kutchire mpaka mkuja madzulo.