1 Samueli 23:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako awiriwo anachita pangano+ pamaso pa Yehova ndipo Davide anakhalabe ku Horesi koma Yonatani anabwerera kwawo. 2 Samueli 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno Davide anamuuza kuti: “Usaope. Ndikusonyeza ndithu chikondi chokhulupirika+ chifukwa cha Yonatani bambo ako. Ndikubwezera malo onse a agogo ako a Sauli ndipo iweyo nthawi zonse uzidya patebulo langa.”+
18 Kenako awiriwo anachita pangano+ pamaso pa Yehova ndipo Davide anakhalabe ku Horesi koma Yonatani anabwerera kwawo.
7 Ndiyeno Davide anamuuza kuti: “Usaope. Ndikusonyeza ndithu chikondi chokhulupirika+ chifukwa cha Yonatani bambo ako. Ndikubwezera malo onse a agogo ako a Sauli ndipo iweyo nthawi zonse uzidya patebulo langa.”+