1 Samueli 27:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma Davide anaganiza kuti: “Tsiku lina Sauli adzandipha ndithu. Chanzeru chimene ndingachite nʼkuthawira+ kudziko la Afilisiti. Ndiyeno Sauli adzasiya kundifunafuna mʼdziko lonse la Isiraeli+ ndipo ndidzapulumuka mʼmanja mwake.”
27 Koma Davide anaganiza kuti: “Tsiku lina Sauli adzandipha ndithu. Chanzeru chimene ndingachite nʼkuthawira+ kudziko la Afilisiti. Ndiyeno Sauli adzasiya kundifunafuna mʼdziko lonse la Isiraeli+ ndipo ndidzapulumuka mʼmanja mwake.”