7 Iweyo ndi ana ako, udindo wanu ndi kugwira ntchito zaunsembe paguwa lansembe komanso pa zinthu zamkati ndi kuseri kwa katani.+ Umenewu ndi utumiki wanu.+ Ndakupatsani utumiki waunsembe kuti ukhale mphatso kwa inu, ndipo munthu wamba aliyense akayandikira pafupi aziphedwa.”+