Numeri 27:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yoswayo aziimirira pamaso pa wansembe Eleazara, ndipo Eleazara azifunsira chigamulo cha Yehova mʼmalo mwa Yoswayo pogwiritsa ntchito maere a Urimu.+ Aliyense azitsatira zimene walamula* kaya ndi Yoswayo, Aisiraeli komanso gulu lonse.” 1 Samueli 30:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako Davide anauza Abiyatara+ wansembe, mwana wa Ahimeleki kuti: “Chonde bweretsa efodi.”+ Choncho Abiyatara anapititsa efodi kwa Davide.
21 Yoswayo aziimirira pamaso pa wansembe Eleazara, ndipo Eleazara azifunsira chigamulo cha Yehova mʼmalo mwa Yoswayo pogwiritsa ntchito maere a Urimu.+ Aliyense azitsatira zimene walamula* kaya ndi Yoswayo, Aisiraeli komanso gulu lonse.”
7 Kenako Davide anauza Abiyatara+ wansembe, mwana wa Ahimeleki kuti: “Chonde bweretsa efodi.”+ Choncho Abiyatara anapititsa efodi kwa Davide.