Salimo 37:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Lola kuti Yehova akutsogolere panjira yako,*+Uzimudalira ndipo iye adzakuthandiza.+ Miyambo 17:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mnzako weniweni amakusonyeza chikondi nthawi zonse,+Ndipo ndi mʼbale amene anabadwa kuti akuthandize pakagwa mavuto.+
17 Mnzako weniweni amakusonyeza chikondi nthawi zonse,+Ndipo ndi mʼbale amene anabadwa kuti akuthandize pakagwa mavuto.+