-
1 Samueli 22:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Anthu onse amene anali pa mavuto, onse amene anali ndi ngongole, ndi onse amene anali ndi madandaulo anasonkhana kwa iye, ndipo iye anakhala mtsogoleri wawo. Amuna onse amene anali naye analipo 400.
-