1 Samueli 25:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Munthuyu dzina lake linali Nabala+ ndipo mkazi wake anali Abigayeli.+ Mkazi wakeyu anali wanzeru ndiponso wokongola, koma mwamunayu anali wouma mtima komanso wopanda khalidwe.+ Iye anali wakubanja la Kalebe.+
3 Munthuyu dzina lake linali Nabala+ ndipo mkazi wake anali Abigayeli.+ Mkazi wakeyu anali wanzeru ndiponso wokongola, koma mwamunayu anali wouma mtima komanso wopanda khalidwe.+ Iye anali wakubanja la Kalebe.+