26 Mbuyanga, ndikulumbira mʼdzina la Yehova, Mulungu wamoyo komanso pamaso panu. Yehova ndi amene wakubwezani+ kuti musapalamule mlandu wa magazi+ komanso kuti musabwezere nokha ndi dzanja lanu. Adani anu ndiponso onse ofuna kukuvulazani mbuyanga, akhale ngati Nabala.