Levitiko 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndipo zotsala pa nsembe yambewu zizikhala za Aroni ndi ana ake,+ chifukwa ndi zopatulika koposa,+ zochokera pansembe zowotcha pamoto zoperekedwa kwa Yehova. Numeri 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Zopereka zonse za zinthu zopatulika,+ zimene Aisiraeli azipereka kwa wansembe, zizikhala zake.+
3 Ndipo zotsala pa nsembe yambewu zizikhala za Aroni ndi ana ake,+ chifukwa ndi zopatulika koposa,+ zochokera pansembe zowotcha pamoto zoperekedwa kwa Yehova.