1 Samueli 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako Elikana anapita kunyumba kwake ku Rama, koma mwanayo anatsala nʼkumatumikira Yehova+ moyangʼaniridwa ndi wansembe Eli. 1 Samueli 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno Samueli ankatumikira+ pamaso pa Yehova ndipo ankavala efodi wansalu,+ ngakhale kuti anali mwana.
11 Kenako Elikana anapita kunyumba kwake ku Rama, koma mwanayo anatsala nʼkumatumikira Yehova+ moyangʼaniridwa ndi wansembe Eli.
18 Ndiyeno Samueli ankatumikira+ pamaso pa Yehova ndipo ankavala efodi wansalu,+ ngakhale kuti anali mwana.