1 Samueli 26:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Abisai anauza Davide kuti: “Lero Mulungu wapereka mdani wanu mʼmanja mwanu.+ Bwanji ndimubaye ndi mkondo nʼkumukhomerera pansi? Ndimubaya kamodzi kokha, sindichita kubwereza kawiri.”
8 Ndiyeno Abisai anauza Davide kuti: “Lero Mulungu wapereka mdani wanu mʼmanja mwanu.+ Bwanji ndimubaye ndi mkondo nʼkumukhomerera pansi? Ndimubaya kamodzi kokha, sindichita kubwereza kawiri.”