Ekisodo 28:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Udzaike Urimu ndi Tumimu*+ mʼchovala pachifuwa chachiweruzo, ndipo zizikhala pamtima pa Aroni akamakaonekera pamaso pa Yehova. Aroni azinyamula pamtima pake zinthu zogwiritsa ntchito poweruza Aisiraeli akamaonekera kwa Yehova nthawi zonse. Numeri 27:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yoswayo aziimirira pamaso pa wansembe Eleazara, ndipo Eleazara azifunsira chigamulo cha Yehova mʼmalo mwa Yoswayo pogwiritsa ntchito maere a Urimu.+ Aliyense azitsatira zimene walamula* kaya ndi Yoswayo, Aisiraeli komanso gulu lonse.”
30 Udzaike Urimu ndi Tumimu*+ mʼchovala pachifuwa chachiweruzo, ndipo zizikhala pamtima pa Aroni akamakaonekera pamaso pa Yehova. Aroni azinyamula pamtima pake zinthu zogwiritsa ntchito poweruza Aisiraeli akamaonekera kwa Yehova nthawi zonse.
21 Yoswayo aziimirira pamaso pa wansembe Eleazara, ndipo Eleazara azifunsira chigamulo cha Yehova mʼmalo mwa Yoswayo pogwiritsa ntchito maere a Urimu.+ Aliyense azitsatira zimene walamula* kaya ndi Yoswayo, Aisiraeli komanso gulu lonse.”