1 Samueli 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma tsopano ufumu wako sukhalitsa.+ Yehova apeza munthu wapamtima pake,+ ndipo Yehova amuika kukhala mtsogoleri wa anthu ake+ chifukwa iwe sunamvere zimene Yehova anakulamula.”+ 1 Samueli 15:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Zitatero, Samueli anamuuza kuti: “Yehova wangʼamba ufumu wa Isiraeli nʼkuuchotsa kwa iwe lero, ndipo adzaupereka kwa munthu wina woyenera kuposa iweyo.+ 1 Samueli 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Samueli anatenga nyanga ya mafuta+ nʼkumudzoza azichimwene ake akuona. Kuyambira tsiku limenelo, mzimu wa Yehova unayamba kuthandiza Davide.+ Kenako Samueli anabwerera ku Rama.+ 1 Samueli 24:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ine ndikudziwa kuti iweyo udzakhala mfumu,+ ndipo ufumu wa Isiraeli udzakhalabe mʼmanja mwako.
14 Koma tsopano ufumu wako sukhalitsa.+ Yehova apeza munthu wapamtima pake,+ ndipo Yehova amuika kukhala mtsogoleri wa anthu ake+ chifukwa iwe sunamvere zimene Yehova anakulamula.”+
28 Zitatero, Samueli anamuuza kuti: “Yehova wangʼamba ufumu wa Isiraeli nʼkuuchotsa kwa iwe lero, ndipo adzaupereka kwa munthu wina woyenera kuposa iweyo.+
13 Samueli anatenga nyanga ya mafuta+ nʼkumudzoza azichimwene ake akuona. Kuyambira tsiku limenelo, mzimu wa Yehova unayamba kuthandiza Davide.+ Kenako Samueli anabwerera ku Rama.+