1 Samueli 30:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Davide anayamba kufunsa Yehova+ kuti: “Kodi ndithamangitse gulu la achifwambali? Kodi ndiwapeza?” Iye anamuyankha kuti: “Inde athamangitse chifukwa uwapeza ndithu ndipo ukapulumutsa anthu amene awatenga.”+ Salimo 34:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mavuto* a munthu wolungama ndi ambiri,+Koma Yehova amamupulumutsa ku mavuto onsewo.+
8 Ndiyeno Davide anayamba kufunsa Yehova+ kuti: “Kodi ndithamangitse gulu la achifwambali? Kodi ndiwapeza?” Iye anamuyankha kuti: “Inde athamangitse chifukwa uwapeza ndithu ndipo ukapulumutsa anthu amene awatenga.”+