1 Samueli 17:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Davide anayamba kufunsa asilikali amene anali naye pafupi kuti: “Kodi munthu amene angaphe Mfilisitiyu nʼkuchititsa kuti Aisiraeli asiye kunyozedwa amupatsa chiyani? Kodi Mfilisiti wosadulidwa ameneyu ndi ndani kuti azinyoza asilikali a Mulungu wamoyo?”+ 2 Samueli 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Musanene zimenezi ku Gati;+Musazilengeze mʼmisewu ya Asikeloni,Chifukwa ana aakazi a Afilisiti akhoza kusangalala,Ana aakazi a anthu osadulidwa akhoza kukondwera.
26 Davide anayamba kufunsa asilikali amene anali naye pafupi kuti: “Kodi munthu amene angaphe Mfilisitiyu nʼkuchititsa kuti Aisiraeli asiye kunyozedwa amupatsa chiyani? Kodi Mfilisiti wosadulidwa ameneyu ndi ndani kuti azinyoza asilikali a Mulungu wamoyo?”+
20 Musanene zimenezi ku Gati;+Musazilengeze mʼmisewu ya Asikeloni,Chifukwa ana aakazi a Afilisiti akhoza kusangalala,Ana aakazi a anthu osadulidwa akhoza kukondwera.