1 Samueli 24:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova aweruze pakati pa ine ndi inu,+ ndipo Yehova abwezere mʼmalo mwa ine,+ koma dzanja langali silidzakuchitirani choipa.+ 1 Samueli 26:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndiyeno Sauli anayankha Davide kuti: “Mulungu akudalitse mwana wanga Davide. Mosakayikira iwe udzachita ntchito zazikulu komanso zidzakuyendera bwino.”+ Zitatero, Davide anachoka ndipo Sauli anabwerera kwawo.+ 2 Samueli 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno Natani anauza Davide kuti: “Munthu ameneyu ndi iweyo. Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Ndinakudzoza kuti ukhale mfumu ya Isiraeli+ ndipo ndinakupulumutsa mʼmanja mwa Sauli.+ Salimo 34:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mngelo wa Yehova amamanga msasa kuzungulira anthu onse amene amaopa Mulungu,+Ndipo amawapulumutsa.+
12 Yehova aweruze pakati pa ine ndi inu,+ ndipo Yehova abwezere mʼmalo mwa ine,+ koma dzanja langali silidzakuchitirani choipa.+
25 Ndiyeno Sauli anayankha Davide kuti: “Mulungu akudalitse mwana wanga Davide. Mosakayikira iwe udzachita ntchito zazikulu komanso zidzakuyendera bwino.”+ Zitatero, Davide anachoka ndipo Sauli anabwerera kwawo.+
7 Ndiyeno Natani anauza Davide kuti: “Munthu ameneyu ndi iweyo. Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Ndinakudzoza kuti ukhale mfumu ya Isiraeli+ ndipo ndinakupulumutsa mʼmanja mwa Sauli.+
7 Mngelo wa Yehova amamanga msasa kuzungulira anthu onse amene amaopa Mulungu,+Ndipo amawapulumutsa.+