1 Samueli 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Samueli anatenga nyanga ya mafuta+ nʼkumudzoza azichimwene ake akuona. Kuyambira tsiku limenelo, mzimu wa Yehova unayamba kuthandiza Davide.+ Kenako Samueli anabwerera ku Rama.+ 2 Samueli 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako amuna a ku Yuda anabwera nʼkudzoza Davide kuti akhale mfumu ya nyumba ya Yuda.+ Iwo anauza Davide kuti: “Anthu a ku Yabesi-giliyadi ndi amene anaika Sauli mʼmanda.” Machitidwe 13:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Atamuchotsa ameneyu, anawapatsa Davide kuti akhale mfumu yawo.+ Iyeyu Mulungu anamuchitira umboni kuti, ‘Ndapeza Davide mwana wa Jese,+ munthu wapamtima panga.+ Ameneyu adzachita zonse zimene ndikufuna.’
13 Samueli anatenga nyanga ya mafuta+ nʼkumudzoza azichimwene ake akuona. Kuyambira tsiku limenelo, mzimu wa Yehova unayamba kuthandiza Davide.+ Kenako Samueli anabwerera ku Rama.+
4 Kenako amuna a ku Yuda anabwera nʼkudzoza Davide kuti akhale mfumu ya nyumba ya Yuda.+ Iwo anauza Davide kuti: “Anthu a ku Yabesi-giliyadi ndi amene anaika Sauli mʼmanda.”
22 Atamuchotsa ameneyu, anawapatsa Davide kuti akhale mfumu yawo.+ Iyeyu Mulungu anamuchitira umboni kuti, ‘Ndapeza Davide mwana wa Jese,+ munthu wapamtima panga.+ Ameneyu adzachita zonse zimene ndikufuna.’