Numeri 27:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yoswayo aziimirira pamaso pa wansembe Eleazara, ndipo Eleazara azifunsira chigamulo cha Yehova mʼmalo mwa Yoswayo pogwiritsa ntchito maere a Urimu.+ Aliyense azitsatira zimene walamula* kaya ndi Yoswayo, Aisiraeli komanso gulu lonse.”
21 Yoswayo aziimirira pamaso pa wansembe Eleazara, ndipo Eleazara azifunsira chigamulo cha Yehova mʼmalo mwa Yoswayo pogwiritsa ntchito maere a Urimu.+ Aliyense azitsatira zimene walamula* kaya ndi Yoswayo, Aisiraeli komanso gulu lonse.”