Yoswa 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma Aefuraimu sanathamangitse Akanani amene ankakhala ku Gezeri.+ Choncho Akananiwo akukhalabe pakati pa Aefuraimu mpaka lero,+ ndipo anayamba kuwagwiritsa ntchito yaukapolo.+
10 Koma Aefuraimu sanathamangitse Akanani amene ankakhala ku Gezeri.+ Choncho Akananiwo akukhalabe pakati pa Aefuraimu mpaka lero,+ ndipo anayamba kuwagwiritsa ntchito yaukapolo.+